LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp17 na. 3 tsa. 16
  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi zidzatheka kuti padziko lapansi pakhale cilungamo ceni-ceni?
  • Kodi Mulungu amakondela?
  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
wp17 na. 3 tsa. 16
Anthu a mitundu yosiyana-siyana

Kodi Baibo Imakamba Ciani?

Kodi zidzatheka kuti padziko lapansi pakhale cilungamo ceni-ceni?

Kodi mungayankhe bwanji?

  • Inde

  • Iyai

  • Kapena

Zimene Baibo imakamba

“Ndikudziŵa bwino kwambili kuti Yehova adzazengela mlandu anthu osautsika. Iye adzacitila cilungamo anthu osauka.” (Salimo 140:12) Ufumu wa Mulungu udzabweletsadi cilungamo ceni-ceni padziko lapansi.

Mfundo zina zimene Baibo imakamba

  • Mulungu amaona zinthu zopanda cilungamo zimene zikucitika, ndipo adzazithetsa.—Mlaliki 5:8.

  • Cilungamo ca Mulungu cidzabweletsa mtendele na citetezo padziko lapansi.—Yesaya 32:16-18.

Kodi Mulungu amakondela?

Ena amakhulupilila kuti Mulungu amadalitsa na kutembelela anthu ena. Ena amakhulupilila kuti Mulungu amaona anthu onse cimodzi-modzi. Nanga imwe muganiza bwanji?

Zimene Baibo imakamba

“Mulungu alibe tsankho. Iye amalandila munthu wocokela mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kucita cilungamo.” (Machitidwe 10:34, 35) Mulungu amaona anthu onse cimodzi-modzi.

Mfundo zina zimene Baibo imakamba

  • Baibo ili na “uthenga wabwino” wopita “kudziko lililonse, fuko lililonse, cinenelo ciliconse, ndi mtundu uliwonse.”—Chivumbulutso 14:6.

Kuti mudziŵe za nthawi pamene cilungamo ceni-ceni cidzakhalako padziko lapansi, onani nkhani 3 m’buku iyi, Zimene Baibulo Ingatiphunzitse, yofalitsidwa na Mboni za Yehova

Buku imeneyi ipezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani