Zamkati
WIKI YA FEBRUARY 27, 2017–MARCH 5, 2017
7 “Khulupilila Yehova Ndipo Cita Zabwino”
Nkhaniyi idzafotokoza mmene lemba la caka ca 2017, ingatilimbikitsile kuyang’ana kwa Yehova kuti atithandize pokumana ndi mavuto. Poona zitsanzo za anthu okhulupilika akale, tidzaona mmene tingaikile cidalilo mwa Yehova kuti adzaticilikiza pocita zimene tingathe polimbana ndi mavuto athu ndi kuthandiza ena.
WIKI YA MARCH 6-12, 2017
12 Muziyamikila Mphatso Yanu ya Ufulu Wosankha Zocita
M’nkhani iyi, tidzaona mmene tingagwilitsile nchito mphatso yathu ya ufulu wosankha m’njila yokondweletsa Mulungu. Tidzaonanso mmene tingalemekezele ufulu wa ena pa zosankha zawo.
WIKI YA MARCH 13-19, 2017
17 N’cifukwa Ciani Kudzicepetsa N’kofunikabe?
WIKI YA MARCH 20-26, 2017
22 Mungakhalebe Wodzicepetsa pa Mayeselo
M’nkhanizi zidzamvetsa tanthauzo la kudzicepetsa. Nkhani yoyamba, idzafotokoza tanthauza la kudzicipetsa ndi zimene sikutanthauza. Yaciŵili idzationetsa mmene tingakhalilebe odzicepetsa pa mayeselo.
WIKI YA MARCH 27, 2017–APRIL 2, 2017
27 ‘Zimenezo Uziphunzitse kwa Amuna Okhulupilika’
Pamene m’badwo wina ucoka ndipo wina ubwela, acinyamata amatenga nchito za acikulile. Nkhaniyi idzafotokoza mmene acinyamata ndi acikulile angathandizilane pa kusintha kumeneku.