Zamkati
WIKI YA APRIL 3-9, 2017
3 Colinga ca Yehova Cidzakwanilitsika
WIKI YA APRIL 10-16, 2017
8 Dipo—‘Mphatso Yangwilo’ Yocokela kwa Atate
Nsembe ya dipo ya Khiristu ni yofunika kwambili pa cikhulupililo cathu, komanso pa colinga ca Yehova ca poyamba cokhudza mtundu wa anthu. Nkhani ziŵilizi, zidzafotokoza cifukwa cake panafunikila dipo, zimene dipolo linakwanilitsa, ndi mmene tingaonetsele kuti timayamikila na mtima wonse mphatso imeneyi yoposa zonse yocokela kwa Atate wathu wakumwamba.
13 Mbili Yanga—Tinaona Cisomo ca Mulungu m’Njila Zambili
WIKI YA APRIL 17-23, 2017
18 Yehova Amatsogolela Anthu Ake
WIKI YA APRIL 24-30, 2017
23 N’ndani Akutsogolela Anthu a Mulungu Masiku Ano?
Kwa zaka zambili, Yehova wakhala akusankha amuna kuti atsogolele. N’cifukwa ciani tingakambe kuti Yehova wakhala akuthandiza amuna amenewo? Nanga tidziŵa bwanji kuti akuthandiza kapolo wokhulupilika ndi wanzelu masiku ano? M’nkhanizi, tidzaphunzila maumboni atatu amene akhala akudziŵikitsa anthu oimilako Mulungu.