Yophunzila
FEBRUARY 2017
NKHANI ZOPHUNZILA WIKI YA: APRIL 3-30, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
KU ETHIOPIA
M’bale aseŵenzetsa Baibo kuuzako ena uthenga wa Ufumu kwa amuna aŵili okhala kumidzi m’dela la mapili ku Ethiopia. Amunawo avala mashawelo a kotoni osoka ndi manja a ku dela limenelo
KULI ANTHU
99,391,000
OFALITSA
10,083
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2015)
25,323
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi ni zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku yakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages