Yophunzila
JULY 2017
NKHANI ZOPHUNZILA: AUGUST 28–SEPTEMBER 24, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
POLAND
Wofalitsa akulalikila mmodzi mwa oseŵenza m’munda wa maapozi ku Grójec.
OFALITSA
119,932
MAPHUNZILO A BAIBO
50,479
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
190,613
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.