Magazini Yophunzila
OCTOBER 2017
NKHANI ZOPHUNZILA: NOVEMBER 27–DECEMBER 24, 2017
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
NIGERIA
Amodzi mwa malo ocitilapo ulaliki wapoyela ku Lagos, mzinda wokhala na anthu ambili mu Africa. Pamalo amenewa, anthu pafupifupi 6 mwezi uliwonse amapempha phunzilo la Baibo.
OFALITSA
370,336
MAPHUNZILO A BAIBO
870,185
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
774,874
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.