Zamkati
3 Mbili Yanga—Kucita Zimene Yehova Watilamula Kumabweletsa Madalitso
WIKI YA NOVEMBER 27, 2017–DECEMBER 3, 2017
7 “Tizisonyezana Cikondi Ceni-ceni m’Zocita Zathu”
Cikondi ceni-ceni cimadziŵikitsa Akhristu oona. Nkhani iyi idzafotokoza zinthu 9 zimene tingacite zoonetsa kuti tili na cikondi “copanda cinyengo.”—2 Akor. 6:6.
WIKI YA DECEMBER 4-10, 2017
12 Coonadi ‘Sicibweletsa Mtendele Koma Lupanga’
Ngati acibululu amatsutsa coonadi, umoyo wa mtumiki wa Yehova ungakhale wovuta. M’nkhani imeneyi, tidzaphunzila zimene tingacite kuti tipilile citsutso ca m’banja.
17 Yosefe wa ku Arimateya Analimba Mtima
WIKI YA DECEMBER 11-17, 2017
21 Mmene Masomphenya a Zekariya Amakukhudzilani
WIKI YA DECEMBER 18-24, 2017
26 Magaleta na Cisoti Cacifumu Zimakutetezani
Nkhani izi zidzafotokoza masomphenya a Zekariya a namba 6, 7, na 8. Masomphenya a namba 6 na 7 adzatithandiza kuyamikila mwayi wathu wotumikila m’gulu loyela la Mulungu. Masomphenya a namba 8, adzatithandiza kuona mmene Yehova amatetezela olambila ake kuti kulambila koona kupitilize.