LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w17 November tsa. 2
  • Zamkati

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zamkati
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
w17 November tsa. 2

Zamkati

WIKI YA DECEMBER 25-31, 2017

3 Muziimba Mosangalala!

Anthu a Yehova akhala akuona kuti kuimba ni mbali yofunika pa kulambila kwawo. Komabe, ena amacita manyazi kuimba pagulu. Tingacite ciani kuti tithetse manyazi n’kumaimba momasuka nyimbo zotamanda Yehova? Nkhani iyi idzafotokoza cifukwa cake tiyenela kuimba mokweza na mosangalala, ndipo idzafotokozanso zina zimene tingacite kuti mau athu azicoka bwino poimba.

WIKI YA JANUARY 1-7, 2018

8 Kodi Mumathaŵila kwa Yehova?

WIKI YA JANUARY 8-14, 2018

13 Tengelani Cilungamo ca Yehova na Cifundo Cake

Tingaphunzilepo zambili pa makonzedwe a mizinda yothaŵilako ya ku Isiraeli wakale. M’nkhani yoyamba, tidzaona zimene munthu amene wacita chimo masiku ano angacite kuti athaŵile kwa Yehova. M’nkhani yaciŵili, tidzaona mmene citsanzo ca Yehova cingatithandizile kukhala na mtima wokhululukila ena, kulemekeza moyo, na kucita zinthu mwacilungamo.

18 “Munthu Wopatsa Mowolowa Manja Adzalandila Mphoto”

WIKI YA JANUARY 15-21, 2018

20 Pewani Kutengela Maganizo a Dziko

WIKI YA JANUARY 22-28, 2018

25 Musalole Ciliconse Kukumanitsani Mphoto

Nkhani ziŵilizi zazikidwa pa malangizo ouzilidwa a Paulo amene analembela Akhristu a ku Kolose. Nkhani yoyamba idzafotokoza zimene tingacite ngati tamva mfundo za dziko zimene zingamveke zokopa. Nkhani yaciŵili idzatikumbutsa mmene tingapewele kucita zinthu zimene zingatilepheletse kudzalandila madalitso amene Yehova walonjeza.

30 Mungacite Ciani Kuti Mujaile mu Mpingo Wanu Watsopano?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani