LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp18 na. 3 masa. 1-2
  • Kodi Mulungu Amakudelani Nkhawa?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mulungu Amakudelani Nkhawa?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
wp18 na. 3 masa. 1-2
Nsanja ya Mlonda, No. 3, 2018 | Kodi Mulungu Amakudelani Nkhawa?

Kodi Mulungu Amakudelani Nkhawa?

Na. 3 2018

© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Pikica ya pacikuto ionetsa munthu wothaŵa kwawo cifukwa ca tsoka la zacilengedwe

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi. Kuti mupeleke copeleka canu, yendani pa webusaiti ya www.jw.org. Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ni Wolamulila wa cilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu na uthenga wabwino wakuti posacedwa Ufumu wa Mulungu udzacotsapo zoipa zonse, na kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsanso anthu kukhulupilila Yesu Khristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha. Ndipo panthawi ino, iye alamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magazini ino yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879, ndipo siiloŵelela m’nkhani zandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani