LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp18 na. 2 tsa. 16
  • “Anthu Ofatsa Adzalandila Dziko Lapansi”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Anthu Ofatsa Adzalandila Dziko Lapansi”
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Coonadi Cingakuthandizileni
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Mungasankhe Mmene Tsogolo Lanu Lidzakhalile
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2021
  • Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
    Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
wp18 na. 2 tsa. 16
Banja

“Anthu Ofatsa Adzalandila Dziko Lapansi”

Ambili a ise taonako zinthu zopanda cilungamo zicitika, anthu abwino ndi osalakwa kupondelezewa na anthu oipa. Kodi nthawi idzafika pamene kuipa na kupanda cilungamo zidzasila?

M’Baibo, Salimo 37 imapeleka yankho na citsogozo kwa ise masiku ano. Onani zimene imakamba pa mafunso ofunika kwambili otsatilawa.

  • Kodi tifunika kucita ciani ngati ena akutipondeleza?—Vesi 1, na 2.

  • N’ciani cidzacitikila anthu oipa?—Vesi 10.

  • Kodi anthu ocita zabwino ali na tsogolo yabwanji?—Vesi 11, na 29.

  • Kodi manje tiyenela kucita ciani?—Vesi 34.

Mau ouzilidwa a mu Salimo 37 aonetselatu kuti anthu amene ‘ayembekezela Yehova, ndi kusunga njila zake’ ali na tsogolo labwino. A Mboni za Yehova ni okonzeka kukuthandizani kuphunzila Baibo. Komanso angakuthandizeni kudziŵa zimene mungacite kuti imwe na okondedwa anu mukhale na tsogolo labwino.

Kuti mudziŵe zambili za tsogolo labwino limene mulungu watilonjeza, yambani maphunzilo a Baibo pogwilitsa nchito bulosha iyi, Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! yolembewa na Mboni za Yehova. Imapezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani