LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp19 na. 1 tsa. 16
  • Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Iye “Amakudelani Nkhawa”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Mmene Coonadi Cingakuthandizileni
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti muvutika?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
  • “Anthu Ofatsa Adzalandila Dziko Lapansi”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
wp19 na. 1 tsa. 16

Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu

ANTHU ENA AMAONA KUTI . . .

Mulungu sasamala za ise ndipo ni wapamwamba kwambili, woyela, komanso wosafikilika.

ZIMENE BAIBO IMAKAMBA

Aŵelenga Baibo

“Yandikilani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikilani.”—Yakobo 4:8.

‘M’tulileni nkhawa zanu zonse, pakuti amakudelani nkhawa.’—1 Petulo 5:7.

KODI TINGACITE CIANI KUTI TIKHALE PA UBWENZI NA MULUNGU?

  • Muzikamba naye.—Salimo 145:18, 19.

  • Muzimumvela.—Salimo 32:8.

  • Muzitsatila malangizo ake.—Miyambo 3:5, 6.

  • Limbikilani kuti mukhale bwenzi lake.—Mateyu 7:7, 8.

Kuti mudziwe zambili zokhudza tsogolo la mtendele limene Mulungu analonjeza, yambani kuphunzila Baibo m’bulosha iyi Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! yolembewa na Mboni za Yehova, imene ipezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani