LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp18 na. 3 tsa. 16
  • Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti muvutika?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti muvutika?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • ONANI ZIMENE BAIBO IMAKAMBA
  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
  • Iye “Amakudelani Nkhawa”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Kodi Baibo Imakamba Ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2017
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
wp18 na. 3 tsa. 16
Anthu akufuna-funa zinthu zimene zapulumuka ku ngozi ya moto m’delalo

Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti muvutika?

Anthu ena amakhulupilila kuti Mulungu saona mavuto awo ndipo sizimukhudza.

ONANI ZIMENE BAIBO IMAKAMBA

  • Mulungu amaona komanso amasamala za ise

    “Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwaculuka padziko lapansi . . . , ndipo zinam’pweteka kwambili mumtima.”—Genesis 6:5, 6.

  • Mulungu adzacotsapo mavuto onse

    “Patsala kanthawi kocepa, woipa sadzakhalakonso. Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo. Koma anthu ofatsa adzalandila dziko lapansi, ndipo adzasangalala ndi mtendele woculuka.”—Salimo 37:10, 11.

  • Zimene Mulungu amakufunilani

    “‘Maganizo anga kwa inu ndikuwadziwa bwino. Ndikuganizila zokupatsani mtendele osati masoka, kuti mukhale ndi ciyembekezo cabwino ndiponso tsogolo labwino,’ watelo Yehova. ‘Mudzaitanila pa ine komanso mudzabwela ndi kupemphela kwa ine ndipo ine ndidzakumvetselani.’”—Yeremiya 29:11, 12.

    “Yandikilani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikilani.”—Yakobo 4:8.

Kuti mudziŵe zambili ponena za cifukwa cake Mulungu amalola kuvutika, onani phunzilo 26 m’buku yakuti, Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! yolembewa na Mboni za Yehova imapezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani