Yophunzila
JANUARY 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: FEBRUARY 26–APRIL 1, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
BOLIVIA
Abale aŵili na azikazi awo akupakila mabuku m’ndeke ku Riberalta, m’cigawo ca Beni. Onsewa ni apainiya. Iwo akupita ku dela lina lakutali la m’dzikoli kukalalikila
OFALITSA
26,081
MAPHUNZILO A BAIBO
42,568
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
75,027
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.