Yophunzila
MARCH 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: APRIL 30–JUNE 3, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
CROATIA
Abale aŵili akugaŵila kapepa kauthenga kwa munthu wogwila nchito yopenta, pa ulalo wa pafupi na malo a citetezo camphamvu ochedwa Kaštilac, amene anamangidwa m’zaka za m’ma 1500 C.E. Malowa ali pafupi na mzinda wa Split
OFALITSA
5,335
MAPHUNZILO A BAIBO
2,123
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2016)
8,434
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.