Zamkati
WIKI YA JUNE 4-10, 2018
3 Njila Yopezela Ufulu Weni-weni
WIKI YA JUNE 11-17, 2018
8 Tumikilani Yehova, Mulungu wa Ufulu
Anthu pa dziko lonse amafunitsitsa kukhala na ufulu waukulu. Kodi Akhristu afunika kuuona bwanji ufulu? Nkhani ziŵilizi zidzafotokoza tanthauzo la ufulu weni-weni, mmene tingaupezele, na mmene tingaseŵenzetsele ufulu wokhala na malile umene tili nawo, kuti tipindule mu umoyo wathu na kupindulitsanso ena. Koposa zonse, tidzaphunzila mmene tingalemekezele Yehova Mulungu, Gwelo la ufulu weni-weni.
13 Amuna a Paudindo —Tengelani Citsanzo ca Timoteyo
WIKI YA JUNE 18-24, 2018
15 Tengelani Yehova —Mulungu Amene Amapeleka Cilimbikitso
WIKI YA JUNE 25, 2018–JULY 1, 2018
20 “Tiyeni Tilimbikitsane, Ndipo Tiwonjezele Kucita Zimenezi”
Nkhanizi zionetsa kuti nthawi zonse Yehova wakhala akulimbikitsa atumiki ake, ndiponso kuti kwa zaka zambili, atumiki akewo akhala akutengela citsanzo cake. Tidzaona cifukwa cake kulimbikitsana n’kofunika maningi masiku ano.
WIKI YA JULY 2-8, 2018
25 Acicepele, Kodi Mumaika Zolinga Zauzimu Patsogolo?
Acicepele mu mpingo wacikhristu amapindula ngati aika mtima wawo pa kucita zinthu zokondweletsa Yehova. Nkhaniyi idzafotokoza zifukwa zake acicepele afunika kuika patsogolo nchito yolalikila, komanso kudziikila zolinga zauzimu akali aang’ono.