Yophunzila
APRIL 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: JUNE 4–JULY 8, 2018
© 2017 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
KYRGYZSTAN
M’bale na mkazi wake, amene na apainiya apadela akulalikila m’dela linalake lakutali ca kufupi na mzinda wa Balykchy
OFALITSA
5,235
OPHUNZILA BAIBO
4,653
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
10,067
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.