Yophunzila
JUNE 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: AUGUST 6–SEPTEMBER 2, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
URUGUAY
Alongo aŵili akulalikila uthenga wofunika kwa mwini shopu ku Montevideo, likulu la dziko la Uruguay
OFALITSA
11,711
MAPHUNZILO A BAIBO
9,001
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
23,426
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.