Yophunzila
July 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: SEPTEMBER 3-30, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
BULGARIA
Pikica iyi ikuonetsa mmene zimakhalila pamene abale akuphunzitsa Baibo akaidi acidwi m’ndende za ku Bulgaria.
OFALITSA
2,475
MAPHUNZILO A BAIBO
2,950
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
5,327
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.