LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w18 July tsa. 2
  • Zamkati

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zamkati
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
w18 July tsa. 2

Zamkati

3 Anadzipeleka na Mtima Wonse —Ku Myanmar

WIKI YA SEPTEMBER 3-9, 2018

7 Kodi Mumafuna Kukhala Wodziŵika kwa Ndani?

Anthu ambili masiku ano amafuna kukhala odziŵika kwa ena m’dziko loipali. M’nkhaniyi tidzakambilana cifukwa cake nthawi zonse tifunika kucita khama kuti tikhalebe wodziŵika kwa Yehova, cifukwa kukhala wodziŵika kwa iye ndiye kofunika kwambili. Tidzakambilananso mmene Yehova amaonetsela kuti amadziŵa anthu ake, ndipo nthawi zina amacita zimenezi m’njila imene iwo sanali kuyembekezela.

WIKI YA SEPTEMBER 10-16, 2018

12 Kodi Maso Anu Amayang’ana kwa Ndani?

M’nkhaniyi, tidzakambilana zimene zinacititsa kuti munthu wokhulupilika Mose ataye mwayi woloŵa m’Dziko Lolonjezedwa. Tidzaonanso mmene tingapewele kucita colakwa ngati cimene Mose anacita.

WIKI YA SEPTEMBER 17-23, 2018

17 “Ndani Ali Kumbali ya Yehova?”

WIKI YA SEPTEMBER 24-30, 2018

22 Ndise Anthu a Yehova

Anthu tonse ndise a Yehova. Ndiye cifukwa cake Yehova amafuna kuti tikhale odzipeleka kwa iye yekha. Anthu ena amacita zinthu zimene Mulungu amazonda, koma n’kumadzinenela kuti amalambila Mulungu. M’nkhani yoyamba, tidzakambilana mfundo zofunika zimene tingaphunzile pa zitsanzo za anthu ochulidwa m’Baibo awa: Kaini, Solomo, Mose na Aroni. M’nkhani yaciŵili, tidzaona njila zosiyana-siyana zimene tingaonetsele kuti timayamikila mwayi wokhala anthu a Yehova.

27 Muzicitila Cifundo Anthu, “Kaya Akhale a Mtundu Wotani”

30 Zimene Mungacite Kuti Kuŵelenga Baibo Kwanu Kukhale Kopindulitsa Komanso Kokondweletsa

32 Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani