Yophunzila
AUGUST 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: OCTOBER 1-28, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
MALAWI
Woyang’anila dela na mkazi wake akonzeka kuti ayambe ulendo wopita kukacezela mpingo wina. Pa njinga zawo anyamula mabuku ophunzilila Baibo, pulojekita, zokuzila mawu, na katundu wawo wina.
OFALITSA
93,412
MAPHUNZILO A BAIBO
145,504
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
315,784
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Ndalama zoyendetsela nchitoyi n’zimene anthu amapeleka mwa kufuna kwawo.
Ngati mufuna kupeleka ndalama zothandizila nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.