Yophunzila
OCTOBER 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: DECEMBER 3-30, 2018
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
VENEZUELA
Amayi ndi ana awo akumwa zozizilitsa ku khosi pamene ali mu ulaliki ku Telares de Palo Grande, mu mzinda wa Caracas
OFALITSA
149,355
MAPHUNZILO A BAIBO
209,866
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
478,266
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mupeleke copeleka canu, yendani pa webusaiti ya www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.