Zamkati
3 1918—Zimene Zinacitika Zaka 100 Zapitazo
WIKI YA DECEMBER 3-9, 2018
WIKI YA DECEMBER 10-16, 2018
Anthu ambili masiku ano amakonda kunama. Kodi bodza linayamba bwanji? Nanga ni bodza liti limene linabweletsa mavuto aakulu kwambili kwa anthu? Tingapewe bwanji kusoceletsedwa? Nanga tingaonetse bwanji kuti timakamba zoona kwa wina na mnzake? Tingaseŵenzetse bwanji Thuboksi yathu ya Zida Zophunzitsila pophunzitsa coonadi mu ulaliki? Nkhani ziŵilizi zidzayankha mafunso amenewa.
17 Mbili Yanga Yehova Anan’dalitsa Kwambili Cifukwa ca Zimene N’nasankha
WIKI YA DECEMBER 17-23, 2018
22 Tizidalila Mtsogoleli Wathu —Khristu
WIKI YA DECEMBER 24-30, 2018
27 Khalanibe na Mtendele wa mu Mtima Olo Pamene Zinthu Zasintha
Pokhala anthu opanda ungwilo, nthawi zambili timakhala na nkhawa kwambili ngati zinthu zasintha mu umoyo wathu kapena m’gulu la Mulungu. Nkhani ziŵilizi zidzatithandiza kukhalabe na mtendele wa mu mtima, komanso kudalila Mtsogoleli wathu, Khristu, pamene zinthu zasintha mosayembekezeleka mu umoyo wathu.