Yophunzila
NOVEMBER 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: DECEMBER 31, 2018–FEBRUARY 3, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
SWEDEN
Ofalitsa mu mzinda wa Stockholm amapeza mpata wocita ulaliki wa m’madzulo m’nyengo yadzuŵa. Iwo amalalikila uthenga wopatsa ciyembekezo kwa madilaiva a taksi, ogulitsa m’mashopu, oseŵenza pa malo ogulitsila mafuta a motoka, komanso kwa anthu ena oseŵenza usiku
OFALITSA
22,418
MAPHUNZILO A BAIBO
10,027
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
34,966
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu.
Ngati mufuna kupeleka zothandizila pa nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.