Yophunzila
DECEMBER 2018
NKHANI ZOPHUNZILA: FEBRUARY 4–MARCH 3, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PIKICA YA PACIKUTO:
MYANMAR
Alongo aŵili apeza anthu ambili oti n’kuwalalikila ku maketi, mu mzinda wa Taunggyi
OFALITSA
4,296
OPHUNZILA BAIBO
4,329
OPEZEKA PA CIKUMBUTSO (2017)
8,659
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu.
Ngati mufuna kupeleka zothandizila pa nchitoyi, yendani pa www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages