LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp19 na. 3 tsa. 16
  • Kodi Pali Ciyembekezo Cakuti Akufa Adzauka?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Pali Ciyembekezo Cakuti Akufa Adzauka?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • ONANI ZIMENE BAIBO IMAKAMBA:
  • N’zotheka Okondedwa Anu Kudzakhalanso na Moyo!
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Akufa Adzauka Ndithu—Sitikaika Konse!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2019
wp19 na. 3 tsa. 16

Kodi Pali Ciyembekezo Cakuti Akufa Adzauka?

Mmodzi wa asayansi amene aonetsedwa kuciyambi, ali na pikica ya banja lokalamba limene laonetsedwa m’nkhani yoyamba

Imfa imakhudza aliyense wa ife. Koma kodi imfa ndiye mapeto a zonse? Kodi akufa basi anaiŵalika? Kodi pali ciyembekezo cakuti akufa adzauka?

ONANI ZIMENE BAIBO IMAKAMBA:

AKUFA SANAIŴALIKE

“Onse ali m’manda acikumbutso . . . adzatuluka.”—Yohane 5:28, 29.

Inde, Mulungu adzaukitsa onse amene akuwambukila.

AKUFA ADZAUKA PA DZIKO LAPANSI

“Kudzakhala kuuka kwa olungama ndi osalungama omwe.”—Machitidwe 24:15.

Anthu ofika m’mabiliyoni adzaukitsidwa ali na ciyembekezo codzakhala na moyo wamuyaya, komanso wamtendele woculuka.

TINGAKHULUPILILEDI KUTI AKUFA ADZAUKA

“[Mulungu] amawelenga nyenyezi zonse, ndipo zonsezo amazichula mayina ake.”—Salimo 147:4.

Popeza Mulungu amatha kuchula nyenyezi iliyonse na dzina lake, si nkhani kwa iye kukumbukila anthu amene afuna kudzawaukitsa.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani