Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
TSANZILANI CIKHULUPILILO CAWO
Yonatani—“Palibe Cimene Cingalepheletse Yehova”
Yonatani pamodzi na mwamuna wina anagonjetsa gulu lalikulu la Afilisti, ndipo zotulukapo zake zinali zosaiŵalika.
(Pitani ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUKHULUPILILA MULUNGU.)
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Ndinagwilizana ndi Bambo Anga Patatha Zaka Zambili
Ali na zaka 14, Renée anacoka panyumba pothaŵa nkhanza za atate ake. Kodi n’ciani cinathandiza Renée na atate ake kugwilizananso patapita zaka zambili?
(Pitani ku Chichewa pambali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MTENDELE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)