Yophunzila
MAY 2019
NKHANI ZOPHUNZILA: JULY 1–AUGUST 4, 2019
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO:
Makolo amateteza ana awo kwa anthu ocitila ana zolaula, mwa kuwaphunzitsa mfundo zoyenelela pankhani yokhudza kugonana. Amacita zimenezi poseŵenzetsa mabuku na mavidiyo amene Gulu la Mulungu lapeleka. (Onani nkhani yophunzila 19, ndime 19-22)