Zina Zimene Zilipo Pa Jw Laibulale Na Pa Jw.Org
KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?
Manja a Octopus Ndi Ogometsa Kwambili
Akatswili acita cidwi na manja ofewa kwambili a octopus, ndipo aganiza zopanga makina amanja othandizila madokota popanga maopaleshoni ovuta kwambili.
(Pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO IMAPHUNZITSA > BAIBULO KOMANSO SAYANSI.)
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
“Ndinkadzikumbila Ndekha Manda”
Óscar amakhulupilila kuti akanapanda kuphunzila Mawu a Mulungu, sembe anafa kale. Óscar ni wa ku El Salvador, ndipo poyamba anali m’gulu la zigaŵenga. Kodi n’ciani cinam’sonkhezela kusintha khalidwe lake?
(Pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO IMAPHUNZITSA > MTENDERE KOMANSO MOYO WOSANGALALA.)