Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
N’cifukwa Ciani Ndimangolankhula Zolakwika?
Ni malangizo ati amene angakuthandizeni kuti muziyamba mwaganiza musanakambe zinthu?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Kodi Ndingatani Ngati Namvela Kuti Mwana Wanga Amavutitsidwa ndi Anzake?
Mfundo zinayi zimene zingakuthandizeni kudziŵa zoyenela kucita mwana wanu akamavutitsidwa.
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA > KULERA ANA.