Yophunzila
NOVEMBER 2019
NKHANI ZOPHUNZILA:DECEMBER 30, 2019–FEBRUARY 2, 2020
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PA CIKUTO:
Pa tsiku la Mwambo Wophimba Macimo, mkulu wa ansembe waciisiraeli anali kuloŵa m’Malo Oyela Koposa atanyamula zofukiza na makala amoto kuti anunkhilitse m’cipindamo na fungo lokoma. Pambuyo pake, anali kuloŵanso m’Malo Oyela Koposa atanyamula magazi a nsembe zophimba macimo (Onani nkhani yophunzila 47, ndime 4)