Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Kucita Zamatsenga Kuli na Vuto Lililonse?
Acicepele ambili amacita cidwi na za ziwanda, vipuku, na za ufiti. Amacitanso cidwi na openda nyenyezi. Kodi pangakhale mavuto otani ngati munthu amacita cidwi na zimenezi?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.
KODI MUKUDZIWA?
Zimene Asayansi Afukula Zikutsimikizila Kuti Mfumu Davide Analikodi
Anthu ena amanena kuti Mfumu Davide kunalibe ndipo nkhani yake ni yongopeka. Kodi asayansi apeza umboni wotani?
Pa jw.org, pitani ku Chichewa pa ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MBIRI KOMANSO BAIBULO > ZINTHU ZAKALE ZOSONYEZA KUTI BAIBULO NDI LOLONDOLA.