Ndandanda ya Mlungu wa November 12
MLUNGU WA NOVEMBER 12
Nyimbo 66 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 15 ndime 1-7, ndi bokosi patsamba 116 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Amosi 1-9 (Mph. 10)
Na. 1: Amosi 3:1-15 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi “Cipangano Catsopano” Cimanena Kuti Dziko Lapansi Lidzakhala Paladaiso Ngati Mmene “Cipangano Cakale” Cimanenela?—rs tsa. 336 ndime 1-3 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Kumvetsa Bwino Lemba la Salimo 51:17 Kungatithandize Bwanji? (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 68
Mph. 10: Ngati Wina Anena Kuti, ‘Simumakhulupilila Yesu.’ Kukambilana kozikidwa pa buku la Kukambitsilana tsamba 433 ndime 1-3. Citani citsanzo cacidule.
Mph. 10: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Kukambilana. Lemba ili liŵelengedwe: Maliko 1:16-20. Kambilanani mmene nkhani ili pa lembali ingatithandizile muulaliki.
Mph. 10: “Sangalalani Ndi Nchito Yanu Yakhama” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo 98 ndi Pemphelo