LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 12/12 tsa. 8
  • Zilengezo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zilengezo
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2012
Utimiki Wathu wa Ufumu—2012
km 12/12 tsa. 8

Zilengezo

◼ Cogaŵila ca mu December: Gaŵilani kalikonse ka tumapepala tauthenga utu: Mavuto Onse a Anthu Adzatha Posachedwapa!, Yehova—Kodi Iye Ndani?, Yesu Kristu—Kodi Iye Ndani?, kapena kakuti Kodi Mufuna Kudziŵa Mayankho Azoona pa Mafunso Aya? Ngati munthuyo ali ndi cidwi, gwilitsilani nchito buku lakuti Baibo Imaphunzitsa, kumuonetsa mmene timacitila phunzilo la Baibo. Kapena gwilitsilani nchito kabuku kakuti Mvetselani kwa Mulungu, kapena kakuti Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. January ndi February: Gaŵilani kalikonse ka tumabuku ta masamba 32 utu: Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kapena kakuti Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu. Pamaulendo obwelelako, gaŵilani buku lakuti Baibo Imaphunzitsa. Ngati kungakhale koyenela kwa munthuyo m’gaŵileni kabuku kakuti Mvetselani kwa Mulungu, kapena kakuti Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. Kenako, yambitsani phunzilo la Baibo.

◼ Cikumbutso ca mu 2014 cidzakhalako pa Mande, April 14.

◼ Ofalitsa amene afuna kucita upainiya mu mwezi wa March 2013 adzakhala ndi mwai wosankha mlingo wa maola 30 kapena 50 m’mwezi umenewo. Ndiponso, ngati woyang’anila dela acezela mpingo mu March, onse amene acita upainiya wothandiza adzapezekapo pa msonkhano wonse wa woyang’anila dela ndi apainiya a nthawi zonse.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani