LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 7/13 tsa. 8
  • Ndandanda ya Mlungu wa August 5

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa August 5
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Tumitu
  • MLUNGU WA AUGUST 5
Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
km 7/13 tsa. 8

Ndandanda ya Mlungu wa August 5

MLUNGU WA AUGUST 5

Nyimbo 77 ndi Pemphelo

□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:

bt mutu 27 ndime 1-9 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibo: Aroma 1-4 (Mph. 10)

Na. 1: Aroma 3:21 mpaka 4:1-8 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: N’cifukwa Ciani Akristu Amadziona Ngati “Alendo Ndiponso Anthu Osakhalitsa M’dzikoli”?—1 Pet. 2:11; 1 Yoh. 2:15-17 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Akristu Oona Adzatetezedwa Bwanji pa Cisautso Cacikulu?—rs tsa. 216 ndime 2-6 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 79

Mph. 10: Zimene Mungakambe Pogaŵila Magazini mu August. Kukambilana. Fotokozani cifukwa cake magazini awa adzakhala okopa anthu a m’gawo lanu. Citani zimenezi kwa tumphindi 30 mpaka 60. Ndiyeno, pa nkhani zoyambilila zogwilizana ndi mutu wa pacikuto ca Nsanja ya Mlonda, pemphani omvela kuti achule funso lodzutsa cidwi limene angafunse poyambitsa makambilano, ndi lemba limene angaŵelenge. Citani cimodzi-modzi ndi Galamukani! komanso ngati nthawi ilola, citaninso cimodzi-modzi ndi nkhani ina imodzi ya mu Nsanja ya Mlonda kapena Galamukani! Citani citsanzo ca mmene mungagaŵilile magazini iliyonse.

Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.

Mph. 10: Tiphunzilapo Ciani? Ŵelengani Luka 5:27-32 ndipo kambilanani mmene lembali lingatithandizile mu utumiki.

Nyimbo 119 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani