LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 9/13 tsa. 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa September 9

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa September 9
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Tumitu
  • MLUNGU WA SEPTEMBER 9
Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
km 9/13 tsa. 1

Ndandanda ya Mlungu wa September 9

MLUNGU WA SEPTEMBER 9

Nyimbo 62 ndi Pemphelo

□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:

bt mutu 28 ndime 16 mpaka 22 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibo: 1 Akorinto 10-16 (Mph. 10)

Na. 1: 1 Akorinto 14:7-25 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: Kodi Zingatheke Bwanji Kuti Munthu Wocimwa ‘Akhazikitse Pansi Mtima wa Yehova’?—2 Mbiri 33:12, 13; Yes. 55:6, 7 (Mph. 5)

Na. 3: N’cifukwa Ciani Sitinganene Kuti Lemba la Yohane 9:1, 2 Limasonyeza Kuti Munthu Amabadwanso Kwinakwake?—rs tsa. 176 ndime 2–tsa. 177 ndime 3 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 89

Mph. 10: Acinyamata—Kodi Moyo Wanu Mudzaugwilitsila Nchito Bwanji?—Gawo 1. Nkhani yocokela m’kapepala kauthenga kakuti Moyo Wanu, ndime 1 mpaka 9. Mwacikondi yamikilani acinyamata obatizika amene akuyesetsa kuika patsogolo Ufumu.

Mph. 10: Zocitika mu Utumiki Pogwilitsila Nchito Kabuku ka Uthenga Wabwino. Kukambitsilana. Pemphani omvela kufotokoza zocitika mu utumiki zogwila mtima zimene akhala nazo pogwilitsila nchito kabuku ka Uthenga Wabwino kuyambitsa phunzilo la Baibo. Citani citsanzo coonetsa mmene mungagwilitsile nchito kabuku kupanga ulendo wobwelelako kwa munthu amene nthawi yoyamba analandila magazini.—Onani Utumiki Wathu wa Ufumu wa March 2013, tsamba 7.

Mph. 10: “Tengelani Citsanzo kwa Aneneli—Amosi.” Mafunso ndi Mayankho.

Nyimbo 96 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani