Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki
Tidzakambilana mafunso otsatilawa pa Sukulu ya Ulaliki mkati mwa mlungu wa October 28, 2013.
1. Kodi kukhala ndi “maganizo a Kristu” kumatanthauzanji? (1 Akor. 2:16) [Sept. 2, w08 7/15 tsa. 27 ndime 7]
2. Kodi ‘timathawa dama’ m’njila ziti? (1 Akor. 6:18) [Sept. 2, w08 7/15 tsa. 27 ndime 9; w04 2/15 tsa. 12 ndime 9]
3. Kodi Paulo anali kutanthauzanji pamene analemba kuti akazi “akhale cete m’mipingo”? (1 Akor. 14:34) [Sept. 9, w12 9/1 tsa. 9, bokosi]
4. Kodi mau a Paulo olembedwa pa 2 Akorinto 1:24 ayenela kukhudza bwanji akulu masiku ano? [Sept. 16, w13 1/15 tsa. 27 ndime 2 mpaka 3]
5. Kodi tingatsatile bwanji mfundo ya pa 2 Akorinto 9:7? [Sept. 23, g 5/08 tsa. 21, bokosi]
6. Kodi tingapindule bwanji tikatsatila langizo la Paulo la pa Agalatiya 6:4? [Sept. 30, w12 12/15 tsa. 13 ndime 18]
7. Kodi ‘kusunga umodzi wathu mwa mzimu’ kumatanthauzanji? (Aef. 4:3) [Oct. 7, w12 7/15 tsa. 28 ndime 7]
8. Kodi Paulo anali kuona bwanji zinthu zimene anazisiya? (Afil. 3:8) [Oct. 14, w12 3/15 tsa. 27 ndime 12]
9. Kodi langizo lakuti “tisapitilize kugona ngati mmene enawo akucitila” limatanthauzanji? (1 Ates. 5:6) [Oct. 21, w12 3/15 tsa. 10 ndime 4]
10. Kodi imfa ya nsembe imene Yesu anafa inali “dipo lokwanila ndendende” m’njila yotani? (1 Tim. 2:6) [Oct. 28, w11 6/15 tsa. 13 ndime 11]