Zilengezo
◼ Cogaŵila ca mu October: Magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! November ndi December: Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni kapena Kodi Mufuna Kudziŵa Mayankho Azoona pa Mafunso Aya? January: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu kapena kamodzi ka tumabuku totsatilatu twa masamba 32: Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalila, kapena Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu!, Mvetselani kwa Mulungu ndi kakuti Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya.
◼ Zofalitsa Zatsopano Zimene Zilipo:
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya—Ichilala
Mvetselani kwa Mulungu—Ichilala
Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu—Zomvetsela pa Intaneti ndi ma CD—Lamba, Mwambwe-Lungu
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya—Zomvetsela pa Intaneti ndi ma CD—Lamba, Mambwe-Lungu