LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 2/14 tsa. 2
  • Ndandanda ya Mlungu wa February 17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa February 17
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Tumitu
  • MLUNGU WA FEBRUARY 17
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 2/14 tsa. 2

Ndandanda ya Mlungu wa February 17

MLUNGU WA FEBRUARY 17

Nyimbo 15 ndi Pemphelo

□ Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 4 ndime 15 mpaka 20 (Mph. 30)

□ Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: Genesis 29 mpaka 31 (Mph. 10)

Na. 1: Genesis 29:21-35 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

Na. 2: Kodi Kuukitsidwa Kudzatanthauza Ciani kwa Anthu Onse?—rs tsa. 110 ndime 1 mpaka tsa. 111 ndime 2 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Ndi Kalankhulidwe Ndiponso Khalidwe Lotani Limene Sililemekeza Ukwati?—lv tsa. 125-126 ndime 10 mpaka 14 (Mph. 5)

□ Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 92

Mph. 10: Muzikhala Aubwenzi Polalikila. Kukumbitsilana kocokela m’buku la Sukulu ya Utumiki tsamba 118, ndime 1, mpaka tsamba 119, ndime 5.

Mph. 5: Kodi Mumagwilitsila Nchito Webusaiti ya jw.org mu Ulaliki? Kukambitsilana. Pemphani omvela kuti afotokoze zocitika zosangalatsa zimene akhala nazo pogwilitsila nchito Webusaiti ya jw.org mu ulaliki. Pomaliza, limbikitsani onse kuti aziuzako ena za Webusaiti yathu nthawi iliyonse mpata ukapezeka. Ngati palibe zocitika za mu utumiki za kumaloko, kambitsilanani nkhani yakuti, “Webusaiti yathu igwilitsileni nchito polalikila,” yocokela mu Utumiki Wathu wa Ufumu wa December 2012.

Mph. 15: “Pangani Nyengo Ino ya Cikumbutso Kukhala Yosangalatsa.” Mafunso ndi mayankho. Pemphani amene akulingalila kucita upainiya wothandiza kuti afotokoze mmene asinthila zinthu paumoyo, kuti aonjezele utumiki mosasamala kanthu za thanzi lao kapena kutangwanika kwao. Pokambitsilana ndime 3, pemphani woyang’anila nchito kuti achule makonzedwe a ulaliki amene mpingo wapanga m’mwezi wa March, April, ndi May.

Nyimbo 8 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani