Zilengezo
◼ Zogaŵila mu February: Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu kapena kamodzi mwa tumabuku twa masamba 32 totsatila: Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kapena kakuti Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu!, Mvetsalani kwa Mulungu, ndi kakuti Mvetselani Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. March ndi April: Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! May: Zimene Baibo Imaphunzitsa kapena kamodzi mwa tumapepala twauthenga totsatila: Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?, Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?, Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?, Kodi Ndani Maka-maka Amene Akulamulila Dzikoli?, Kodi Mavuto Adzathadi?, ndi Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?
◼ Nkhani yapadela m’nyengo ya Cikumbutso ca 2014 idzakhala ndi mutu wakuti, “N’cifukwa Ciani Mulungu Wacikondi Walola Anthu Kuvutika?”