Ndandanda ya Mlungu wa March 17
MLUNGU WA MARCH 17
Nyimbo 113 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 6 ndime 1-6 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Genesis 43-46 (Mph. 10)
Na. 1: Genesis 44:18-34 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Ndi Anthu Enanso Ati Amene Adzaukitsidwa Kuti Akhale Ndi Moyo Padziko Lapansi?—rs tsa. 113 ndime 1-5 (Mph. 5)
Na. 3: N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupitiliza Kudalila Yehova?—bh tsa. 164 mpaka 165 ndime 1-4 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 61
Mph. 15: Khalani Osamala Polalikila. Nkhani yokambitsilana yocokela m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 197, ndime 1, mpaka tsamba 199, ndime 4. Citani citsanzo coonetsa wofalitsa akuyankha mosasamala munthu wotsutsa. Kenako citani citsanzo cina coonetsa wofalitsa akuyankha mosamala kwambili munthu wotsutsa.
Mph. 15: “Kodi Mudzatengako Mbali?” Mafunso ndi mayankho. Pemphani omvela kuti afotokoze mmene aziŵelengela Malemba amene asankhidwa panyengo ya Cikumbutso. Fotokozani zimene mwakonza kucita pampingo wanu panyengo ya Cikumbutso.
Nyimbo 8 ndi Pemphelo