LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 6/14 tsa. 8
  • Zocitika Zokhudza Ulaliki

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zocitika Zokhudza Ulaliki
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 6/14 tsa. 8

Zocitika Zokhudza Ulaliki

Mu November ofalitsa anagaŵila tumapepala twauthenga ndi tumabuku toposa 540,000.

Mu January tinaona kuti mpingo umodzi pa mipingo 5 iliyonse unatha kugwilitsila nchito malo ao a pa jw.org. Ndipo ndife okondwela kwambili kuti potumiza lipoti la utumiki wakumunda mipingo inagwilitsila nchito njila imeneyi. Mungagwilitsile nchito webu saiti imeneyi kuitanitsa mabuku, kulandila ndi kutumiza makalata ku ofesi ya nthambi ndiponso potumiza cidziŵitso ciliconse cofunika. Kodi mpingo wanu ukugwilitsila nchito webusaiti imeneyi?

Maphunzilo: Ndife okondwela kulengeza kuti akulu oposa 9,700 anaphunzitsidwa pa Sukulu ya Akulu a Mpingo ya mlungu umodzi. M’mwezi wa May, abale ndi alongo amene anali pa Sukulu ya Oyang’anila Oyendela ndi Akazi Ao ya nambala 10 anamaliza maphunzilo ao. M’mwezi umenewu ophunzila a kalasi ya nambala 3 ya Sukulu Yophunzitsa Baibulo ya Akristu Ali Pabanja naonso anamaliza maphunzilo ao ndipo anatumizidwa kukatumikila ku maiko angapo a ku Southern Africa.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani