LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 2/15 tsa. 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa February 9

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa February 9
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Tumitu
  • MLUNGU WA FEBRUARY 9
Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
km 2/15 tsa. 1

Ndandanda ya Mlungu wa February 9

MLUNGU WA FEBRUARY 9

Nyimbo 9 ndi Pemphelo

Phunzilo la Baibulo la Mpingo

cl mutu. 5 ndime 1-8 (Mph. 30)

Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: Oweruza 11-14 (Mph. 8)

Na. 1: Oweruza 13:15-25 (Mph. 3 kapena zocepelapo)

Na. 2: Anasi—Mutu: Kutsutsana ndi Coonadi Kulibe Phindu Lililonse—w12 4/1 tsa. 9 ndime 4-6 (Mph. 5)

Na. 3: Kodi Baibulo ndi Loona pa Nkhani za Sayansi?—igw-CIN tsa. 7 ndime 1-3 (Mph. 5)

Msonkhano wa Nchito:

Lemba la Mwezi: Khalani “Odzipeleka pa Nchito Zabwino.”—Tito 2:14.

Nyimbo 54

Mph. 15: “N’cifukwa Ciani Tiyenela Kukhala ‘Odzipeleka pa Nchito Zabwino’?” Kukambitsilana. Mufotokozenso mfundo za mu Nsanja ya Olonda ya June 1, 2002, tsamba 23, ndime 17-19.

Mph. 15: “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Ulaliki Wapoyela M’gawo la Mpingo Wanu.” Kukambitsilana. Pemphani ofalitsa kusimba zocitika za kudelalo zoonetsa mmene ena alabadilila ulaliki wapoyela. Citani citsanzo cacidule coonetsa mmene mungacitile ulaliki umenewu.

Nyimbo 33 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani