Zilengezo
◼ Cogaŵila mu February: Uthenga Wocokela kwa Mulungu. March ndi April: Gaŵilani magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani! May: Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni kapena kamodzi ka tumapepala twa uthenga utu: Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?, Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?, Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?, Kodi Ndani Maka-maka Amene Akulamulila Dzikoli?, Kodi Mavuto adzathadi?, ndi Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?
◼ Nkhani yapadela m’nyengo ya cikumbutso ca 2015 idzakhala ya mutu wakuti: “Lonjezo la Banja la Cimwemwe Cosatha.”
◼ Cofalitsa Cimene Cilipo: Imbilani Yehova (sny55)—Mambwe-Lungu.