Ndandanda ya Mlungu wa March 23
MLUNGU WA MARCH 23
Nyimbo 119 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 7 ndime 1-8 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Samueli 10–13 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Samueli 11:1-10 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Baibulo Linalosela Ciani za Nthawi Yathu Ino?—igw-CIN tsa. 12 ndime 1-4 (Mph. 5)
Na. 3: Azariya—Mutu: Anali ndi Cikhulupililo Colimba Kuyambila Ali Mwana—w05 7/15 tsa. 27 ndime 5-8 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: ‘Khalani Okonzeka Kugwila Nchito Iliyonse Yabwino.’—Tito 3:1.
Nyimbo 20
Mph. 30: “Misonkhano Yokonzekela Ulaliki Imene Imakwanilitsa Colinga Cake.” Mafunso ndi mayankho.
Nyimbo 32 ndi Pemphelo