Ndandanda ya Mlungu wa June 1
MLUNGU WA JUNE 1
Nyimbo 13 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 10 ndime 8-17 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 2 Samueli 16-18 (Mph. 8)
Na. 1: 2 Samueli 17:14-20 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Boazi—Mutu: Khalani Oyela m’Makhalidwe ndi Okonzeka Kusenza Udindo wa m’Malemba—(w12 10/1 tsa. 22 ndime 1-tsa. 24 ndime 1) (Mph. 5)
Na. 3: Cuma Canu Mungacisamalile Bwanji?—(igw-CIN tsa. 21 ndime 1-4) (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: Thandizani anthu a mitundu yonse kudziŵa coonadi molondola.—1 Tim. 2:3, 4.
Nyimbo 36
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu June. Kukambilana. Yambani ndi citsanzo coonetsa mmene tingagaŵile magazini, pogwilitsila nchito maulaliki aŵili a citsanzo. Pambuyo pake mukambilane maulaliki onse a citsanzo.
Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.
Mph. 10: Tinacita Zotani? Kukambilana. Pemphani omvela kuti akambe mmene anapindulila ndi nkhani yakuti “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Munthu Amene Amakamba Cinenelo Cina.” Pemphani gulu kuti lifotokoze zocitika zosangalatsa.
Nyimbo 25 ndi Pemphelo