Ndandanda ya Mlungu wa August 3
MLUNGU WA AUGUST 3
Nyimbo 63 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 13 ndime 11-18 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 1 Mafumu 18-20 (Mph. 8)
Na. 1: 1 Mafumu 18:30-40 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Debora —Mutu: Akazi Okhulupilika Amatamanda Yehova—w14 8/15 tsa. 8 ndime 12 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Baibulo Lingathandize Bwanji Ana?—igw-CIN tsa. 27 ndime 1-2 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Pitani mukaphunzitse anthu.”—Mat. 28:19, 20.
Nyimbo 130
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu August. Kukambilana. Yambani ndi citsanzo coonetsa mmene tingagaŵile magazini pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo amene tapatsidwa. Ndiyeno kambilanani ulaliki uliwonse kucokela kuciyambi mpaka kumapeto.
Mph. 10: Pindulani ndi Kuphunzila Malemba Tsiku ndi Tsiku. Kukambilana. Yambani mwa kukamba nkhani ya mphindi 5 yozikidwa pa lemba la caka ca 2015. Pambuyo pake, pemphani ofalitsa kuti akambe nthawi imene amaphunzila malemba tsiku lililonse. Ndiyeno limbikitsani onse kuti azigwilitsila nchito bwino kabuku ka Kuphunzila Malemba Tsiku ndi Tsiku.
Mph. 10: Zosoŵa za pampingo.
Nyimbo 26 ndi Pemphelo