LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 9/15 tsa. 1
  • Ndandanda ya Mlungu wa September 14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa September 14
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Tumitu
  • MLUNGU WA SEPTEMBER 14
Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
km 9/15 tsa. 1

Ndandanda ya Mlungu wa September 14

MLUNGU WA SEPTEMBER 14

Nyimbo 50 ndi Pemphelo

Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

cl mutu 15 ndime 11-19 (Mph. 30)

Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: 2 Mafumu 16-18 (Mph. 8)

Na. 1: 2 Mafumu 17:12-18 (Mph. 3 kapena zocepelapo)

Na. 2: Mungacite Ciani Kuti Mupindule Kwambili Pamene Muŵelenga Baibulo?—(igw-CIN tsa. 32) (Mph. 5)

Na. 3: Ebedi-meleki—Mutu: Khalani Olimba Mtima Ndipo Muzilemekeza Atumiki a Yehova—(w13 1/15 tsa. 9 ndime 12) (Mph. 5)

Msonkhano wa Nchito:

Lemba la Mwezi: “Kucitila umboni mokwanila za uthenga wabwino.”—Machitidwe 20:24.

Nyimbo 23

Mph. 10: “Kucitila Umboni Mokwanila za Uthenga Wabwino.” Nkhani yozikidwa pa lemba la mwezi ndi m’buku la Kuchitira Umboni, mutu 1, ndime 1-11.—Machitidwe 20:24.

Mph. 20: “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila m’Gawo la Malonda.” Kukambilana. Citani citsanzo cacidule ca mbali ziŵili. Mbali yoyamba, wofalitsa asaonetse luso la kuzindikila polalikila wamalonda. Koma mbali yaciŵili, wofalitsa aonetse luso la kuzindikila. Pemphani omvela kuti afotokoze cifukwa cake citsanzo caciŵili ndi cogwila mtima kwambili.

Nyimbo 96 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani