LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 March tsa. 4
  • March 14-20

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 14-20
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 March tsa. 4

March 14-20

YOBU 1-5

  • Nyimbo 89 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yobu Anakhalabe Wokhulupilika Pamene Anali Kuyesedwa”: (Mph. 10)

    • [Onetsani vidiyo yofotokoza Mfundo Zokhudza Buku la Yobu. Ngati n’zosatheka kuonelela vidiyo, yambani kukamba nkhani yakuti “Yobu Anakhalabe Wokhulupilika Pamene Anali Kuyesedwa.”]

    • Yobu 1:8-11—Satana anakaikila kukhulupilika kwa Yobu (w11–CN 5/15 17 ndime 6-8; w09–CN 4/15 3 ndime 3-4)

    • Yobu 2:2-5—Satana anakaikila zakuti anthu onse angakhale okhulupilika (w09–CN 4/15 4 ndime 6)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Yobu 1:6; 2:1—Ndani ankaloledwa kuonekela kwa Yehova? (w06–CN 3/15 13 ndime 6)

    • Yobu 4:7, 18, 19—Ndi maganizo olakwika ati amene Elifazi anauza Yobu? (w14–CIN 3/1 12 ndime 3; w05–CN 9/15 26 ndime 4-5; w95–CN 2/15 27 ndime 5-6)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Yobu 4:1-21 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya 2016 Na.2 pacikuto. Yalani maziko a ulendo wobwelelako. (Mph. 2 kapena zocepelapo)

  • Ulendo wobwelelako: Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya 2016 Na.2 pacikuto. Yalani maziko a ulendo wina wobwelelako. (Mph. 4 kapena zocepelapo)

  • Phunzilo la Baibulo: fg phunzilo 2 ndime 2-3 (Mph. 6 kapena zocepelapo)

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 88

  • Pewani Kusonkhezeledwa ndi Anzanu: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Stand Up to Peer Pressure! (Pitani polemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACINYAMATA. Ngati n’zosatheka kambani mfundo za m’buku la Zimene Acinyamata Amafunsa Voliyamu 2 mutu 15 mas. 129-130.) Mukatsiliza, funsani mafunso otsatilawa: Kodi ana amakumana ndi mayeselo otani kusukulu? Kodi angagwilitsile nchito bwanji mfundo ya pa Ekisodo 23:2? Ndi njila zinai ziti zimene zingawathandize kulimbana ndi ziyeso ndi kukhalabe okhulupilika? Pemphani acinyamata kuti afotokoze zocitika zosangalatsa.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 11 ndime 1-11 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zimene Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 133 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani