LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsa. 8
  • Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka Zoposa 100

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka Zoposa 100
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • “Ufumu Wanu Udze”—Pemphelo Limene Anthu Ambili Amapeleka
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciyani?
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Kodi Ufumu wa Mulungu Uli mu Mtima Mwanu?
    Kuyankha Mafunso Okhudza Baibo
  • Kodi Baibulo Imakamba Ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2016
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 June tsa. 8

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka Zoposa 100

Galimoto yokhala ndi zokuzila mawu, Mboni za Yehova ziseŵenzetsa zikwangwani poitanila anthu ku nkhani ya onse

Amene afuna kukhala nzika za Ufumu wa Mulungu ayenela kudziŵa zinthu zokhudza Ufumuwo, ndi zimene wakwanitsa kucita. N’cifukwa ciani? Kucita zimenezi kudzawathandiza kukhala ndi cikhulupililo cakuti Ufumu wa Mulungu ukulamulila. Ndipo kudzawasonkhezela kuuzako ena za Ufumu wa Mulungu.’ (Sal. 45:1; 49:3) Pamene muonelela vidiyo yakuti Ufumu wa Mulungu Wakwanitsa Zaka Zoposa 100, pezani mayankho a mafunso otsatila:

  1. N’cifukwa ciani “Sewelo la Pakanema la Cilengedwe” linali dalitso kwa amene anaionelela?

  2. Kodi wailesi inali kuseŵenzetsedwa bwanji kuti ithandize pa kufalitsa uthenga wabwino?

  3. Ni njila zina ziti zimene anali kuseŵenzetsa polalikila uthenga wabwino? Nanga panakhala zotulukapo zabwanji?

  4. Kodi masukulu ophunzitsa ulaliki apita bwanji patsogolo pa zaka zonsezi?

  5. Ni maphunzilo otani amene anakonzedwela oloŵa Sukulu ya Gileadi?

  6. Kodi misonkhano ya cigawo yathandiza bwanji pa nkhani yophunzitsa anthu a Yehova?

  7. N’ciani cimakucititsani kutsimikizila kuti Ufumu wa Mulungu ukulamulila?

  8. Kodi timaonetsa bwanji kuti timacilikiza Ufumu wa Mulungu?

Kuyambila mlungu wa September 19, 2016, pa Phunzilo la Baibulo la Mpingo tidzayamba kuphunzila buku lakuti Ufumu wa Mulungu Ukulamulila

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani