LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 June tsa. 6
  • June 27–July 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 27–July 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 June tsa. 6

June 27–July 3

MASALIMO 52-59

  • Nyimbo 38 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Umutulile Yehova Nkhawa Zako”: (Mph. 10)

    • Sal. 55:2, 4, 5, 16-18—Nthawi zina, Davide anali kukhala ndi nkhawa (w06 6/1 11 ndime 3 CN; w96 4/1 27 ndime 2 CN)

    • Sal. 55:12-14—Mwana wa Davide kuphatikizapo mnzake wa pamtima anamuukila (w96 4/1 30 ndime 1 CN)

    • Sal. 55:22—Davide anadalila thandizo la Yehova (w06 6/1 11 ndime 4 CN; w99 3/15 22-23 CN)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 56:8—Kodi mau akuti “sungani misozi yanga m’thumba lanu lacikopa” atanthauza ciani? (w09 6/1 29 ndime 1 CN; w08 10/1 26 ndime 3 CN)

    • Sal. 59:1, 2—Kodi zimene zinacitikila Davide zitiphunzitsa ciani pankhani ya pemphelo? (w08 3/15 14 ndime 13 CN)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 52:1– 53:6

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Gaŵilani kamodzi ka tumapepala twauthenga. Fotokozani za cidindo cimene cili kothela kwa kapepala kauthenga.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Citani citsanzo ca mmene mungacitile ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala kauthenga.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 3 ndime 2-3—Tsilizani mwa kukamba mau oonetsa kuti mufuna kutambitsa vidiyo ya pa jw.org yakuti, Tingatsimikizile Bwanji Kuti Baibulo Limakamba Zoona?

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 56

  • Zosoŵa za pampingo: (Mph. 7)

  • “Mulungu Ndiye Mthandizi Wanga”: (Mph. 8) Kukambilana. Pelekani mwai kwa abale ndi alongo wakuti ayankhepo pa mafunso amene alipo kuti onse apindule. (Aroma 1:12) Limbikitsani ofalitsa kuti aziseŵenzetsa Buku Lofufuzila Nkhani kuti apeze thandizo la m’Mau a Mulungu akakumana ndi mavuto.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 18 ndime 14-21, ndi kubwelelamo pa tsa. 161

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 121 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani